Numeri 26:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Amenewa ndiwo anali mabanja a Nafitali+ potsata fuko lawo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,400.+
50 Amenewa ndiwo anali mabanja a Nafitali+ potsata fuko lawo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,400.+