Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+
29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+