Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+

  • Genesis 49:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+

  • Yoswa 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo Yehova anapereka adaniwo m’manja mwa Aisiraeli.+ Chotero anayamba kuwapha ndi kuwathamangitsa mpaka kukafika kumzinda wa anthu ambiri wa Sidoni,+ ku Misirepotu-maimu+ ndi kuchigwa cha Mizipe+ kum’mawa. Anapitiriza kuwapha moti panalibe amene anapulumuka.+

  • Oweruza 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Asidoni,+ Aamaleki+ ndi Amidiyani+ atakuponderezani,+ sindinakupulumutseni m’manja mwawo mutafuulira kwa ine?

  • Oweruza 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho amuna asanu aja anapitiriza ulendo wawo ndipo anafika kumzinda wa Laisi.+ Kumeneko anaona kuti anthu a mumzindawo anali kukhala mosadalira aliyense, malinga ndi chikhalidwe cha Asidoni. Iwo anali kukhala phee, mosatekeseka,+ ndipo panalibe amene anawagonjetsa n’kumawachitira nkhanza kapena kuwavutitsa m’dzikolo. Kuwonjezera apo, anali kukhala kutali kwambiri ndi Asidoni+ ndipo sanali kuyenderana ndi anthu a m’madera ena.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena