Numeri 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Mulungu anapsa mtima poona kuti Balamu akupita, moti mngelo wa Yehova anaima pamsewu kuti amutchingire njira.+ Balamuyo anali pabulu wake, ndipo anali ndi anyamata ake awiri.
22 Tsopano Mulungu anapsa mtima poona kuti Balamu akupita, moti mngelo wa Yehova anaima pamsewu kuti amutchingire njira.+ Balamuyo anali pabulu wake, ndipo anali ndi anyamata ake awiri.