Oweruza 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu. 2 Samueli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu.
13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.