Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti,

  • 1 Mafumu 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho Basa mfumu ya Isiraeli anapita kukaukira Yuda. Kenako anayamba kumanga mpanda wolimba kwambiri kuzungulira mzinda wa Rama,+ kuti anthu asamapite kwa Asa mfumu ya Yuda kapena kubwera kuchokera kwa Asa.+

  • Nehemiya 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Hazori, Rama,+ Gitaimu,+

  • Yeremiya 40:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya, pamene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anamumasula ku Rama.+ Yeremiya anali womangidwa maunyolo a m’manja pamene Nebuzaradani anamutenga pakati pa anthu a ku Yerusalemu ndi a ku Yuda amene anali kupita ku ukapolo ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena