Mateyu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Madzulowo,+ mwinimunda wa mpesa uja anauza kapitawo wake kuti, ‘Itana antchito aja uwapatse malipiro awo,+ kuyambira omalizira, kutsiriza ndi oyambirira.’
8 “Madzulowo,+ mwinimunda wa mpesa uja anauza kapitawo wake kuti, ‘Itana antchito aja uwapatse malipiro awo,+ kuyambira omalizira, kutsiriza ndi oyambirira.’