Oweruza 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu.
2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu.