Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Yehova anamuuza kuti: “Mtendere ukhale nawe.+ Usachite mantha.+ Suufa.”+

  • 1 Samueli 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’bale wangayo mukamuuze kuti, ‘Mtendere ukhale nawe+ pamodzi ndi onse a m’nyumba yako ndi zonse zimene uli nazo.

  • 1 Mbiri 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Poyankha, Amasai mkulu wa asilikali 30 anagwidwa ndi mzimu,+ ndipo anati:

      “Ifetu ndife anthu anu, inu a Davide, ndipotu tili kumbali yanu,+ inu mwana wa Jese.

      Mtendere ukhale nanu, ndiponso mtendere ukhale ndi iye amene akukuthandizani,

      Pakuti Mulungu wanu wakuthandizani.”+

      Choncho Davide anawalandira ndi kuwaika pakati pa atsogoleri a asilikali.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena