Genesis 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Paja ine ndili ndi ana aakazi awiri amene sanagonepo ndi mwamuna.+ Bwanji ndikutulutsireni amenewo kuti muchite nawo zimene mukufuna.+ Koma amuna okhawa musawachite chilichonse ayi,+ chifukwa abwera m’nyumba* mwanga kuti adzatetezedwe.”+
8 Paja ine ndili ndi ana aakazi awiri amene sanagonepo ndi mwamuna.+ Bwanji ndikutulutsireni amenewo kuti muchite nawo zimene mukufuna.+ Koma amuna okhawa musawachite chilichonse ayi,+ chifukwa abwera m’nyumba* mwanga kuti adzatetezedwe.”+