Yoswa 15:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero. Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+
63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero.
21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+