Oweruza 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+ Hoseya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu ana a Isiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira m’masiku a Gibeya+ ndipo anthu anapitirizabe kuchita machimo kumeneko. Nkhondo ya ku Gibeya yomenyana ndi anthu osalungama sinawawononge onse.+
12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+
9 “Inu ana a Isiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira m’masiku a Gibeya+ ndipo anthu anapitirizabe kuchita machimo kumeneko. Nkhondo ya ku Gibeya yomenyana ndi anthu osalungama sinawawononge onse.+