Levitiko 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense wa inu akadzachita chilichonse mwa zinthu zonse zonyansazi, anthu ochita zimenezi adzaphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.+ Oweruza 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera. Oweruza 20:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamapeto pake, ana a Benjamini onse amene anaphedwa pa tsikulo, anakwana amuna 25,000 ogwira lupanga.+ Onsewa anali amuna amphamvu zawo.
29 Aliyense wa inu akadzachita chilichonse mwa zinthu zonse zonyansazi, anthu ochita zimenezi adzaphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.+
15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera.
46 Pamapeto pake, ana a Benjamini onse amene anaphedwa pa tsikulo, anakwana amuna 25,000 ogwira lupanga.+ Onsewa anali amuna amphamvu zawo.