Oweruza 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano ana a Isiraeli anali atagwirizana ndi amuna amene anabisala aja kuti akafukize utsi mumzindamo kuti ukhale chizindikiro.+
38 Tsopano ana a Isiraeli anali atagwirizana ndi amuna amene anabisala aja kuti akafukize utsi mumzindamo kuti ukhale chizindikiro.+