Oweruza 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi+ anakhala mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Mayi ake anali hule,+ ndipo bambo ake omubereka anali Giliyadi. Oweruza 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera.
11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi+ anakhala mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Mayi ake anali hule,+ ndipo bambo ake omubereka anali Giliyadi.
15 Choncho ana a Benjamini anasonkhana pamodzi tsiku limenelo kuchokera m’mizinda. Iwo anali amuna ogwira lupanga okwanira 26,000,+ osawerengera anthu okhala m’Gibeya, mmene anasonkhanitsa amuna 700 osankhidwa mwapadera.