Oweruza 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano popeza kuti ife talumbira+ pali Yehova kuti sitiwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo,+ tichita chiyani ndi anthu amene atsala opanda akaziwa?”
7 Tsopano popeza kuti ife talumbira+ pali Yehova kuti sitiwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo,+ tichita chiyani ndi anthu amene atsala opanda akaziwa?”