Oweruza 20:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi. Oweruza 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pakati pa anthu okhala ku Yabesi-giliyadi+ anapeza atsikana 400, anamwali+ amene anali asanagonepo ndi mwamuna. Amenewa anawabweretsa ku msasa ku Silo,+ m’dziko la Kanani.
47 Koma amuna 600 anatembenuka ndi kuthawira kuchipululu kuthanthwe la Rimoni. Iwo anapitiriza kukhala kuthanthwe la Rimoni+ kwa miyezi inayi.
12 Koma pakati pa anthu okhala ku Yabesi-giliyadi+ anapeza atsikana 400, anamwali+ amene anali asanagonepo ndi mwamuna. Amenewa anawabweretsa ku msasa ku Silo,+ m’dziko la Kanani.