Oweruza 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atafika kwa Egiloni mfumu ya Mowabu,+ anapereka msonkho umene anabweretsa. Komatu Egiloni anali munthu wonenepa kwambiri. Salimo 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mitima yawo siimva chisoni,*+Ndipo amalankhula modzikuza ndi pakamwa pawo.+
17 Atafika kwa Egiloni mfumu ya Mowabu,+ anapereka msonkho umene anabweretsa. Komatu Egiloni anali munthu wonenepa kwambiri.