Yoswa 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Kalebe anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi n’kuulanda, ndithu ndim’patsa mwana wanga Akisa,+ kuti akhale mkazi wake.”
16 Kenako Kalebe anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi n’kuulanda, ndithu ndim’patsa mwana wanga Akisa,+ kuti akhale mkazi wake.”