Genesis 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo iye anati: “Ndikutemberera Kanani.+ Akhale kapolo wapansi kwambiri kwa abale ake.”+ Deuteronomo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzakuchititsa kukhala kumutu osati kumchira. Pamenepo udzangokhala pamwamba+ ndipo sudzakhala m’munsi, chifukwa ukumvera malamulo+ a Yehova Mulungu wako amene ndikukupatsa lero kuti uwasunge ndi kuwatsatira.
13 Yehova adzakuchititsa kukhala kumutu osati kumchira. Pamenepo udzangokhala pamwamba+ ndipo sudzakhala m’munsi, chifukwa ukumvera malamulo+ a Yehova Mulungu wako amene ndikukupatsa lero kuti uwasunge ndi kuwatsatira.