Numeri 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anakhala ndi ziweto zambiri, zankhaninkhani. Iwo anayamba kusirira dziko la Yazeri+ ndi la Giliyadi, ndipo deralo linalidi malo abwino a ziweto. Numeri 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mizinda ya ana anu aang’ono, ndi makola amiyala a ziweto zanu, mangani. Koma zonse zimene mwalonjeza muchitedi.”+
32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anakhala ndi ziweto zambiri, zankhaninkhani. Iwo anayamba kusirira dziko la Yazeri+ ndi la Giliyadi, ndipo deralo linalidi malo abwino a ziweto.
24 Mizinda ya ana anu aang’ono, ndi makola amiyala a ziweto zanu, mangani. Koma zonse zimene mwalonjeza muchitedi.”+