Numeri 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ataona Akeni,+ anapitirizanso mawu ake a ndakatulo, kuti:“Mokhala mwanu ndi mokhazikika, malo okhala inu ali pathanthwe. Oweruza 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zili choncho, Hiberi+ Mkeni anapatukana ndi Akeni,+ ana a Hobabu mpongozi wa Mose,+ ndipo anamanga hema wake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.
21 Iye ataona Akeni,+ anapitirizanso mawu ake a ndakatulo, kuti:“Mokhala mwanu ndi mokhazikika, malo okhala inu ali pathanthwe.
11 Zili choncho, Hiberi+ Mkeni anapatukana ndi Akeni,+ ana a Hobabu mpongozi wa Mose,+ ndipo anamanga hema wake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.