Yoswa 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera. Yoswa 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+
15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera.
19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+