Deuteronomo 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ng’ombe yako idzaphedwa iwe ukuona, koma nyama yake sudzadyako. Bulu wako adzalandidwa ndi achifwamba iwe ukuona, ndipo sudzamuonanso. Nkhosa yako idzaperekedwa kwa adani ako, koma sipadzakhala wokupulumutsa.+ Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ Mika 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mudzabzala mbewu koma simudzakolola. Mudzaponda maolivi koma simudzadzola mafuta. Mudzaponda mphesa koma simudzamwa vinyo wotsekemera.*+
31 Ng’ombe yako idzaphedwa iwe ukuona, koma nyama yake sudzadyako. Bulu wako adzalandidwa ndi achifwamba iwe ukuona, ndipo sudzamuonanso. Nkhosa yako idzaperekedwa kwa adani ako, koma sipadzakhala wokupulumutsa.+
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
15 Mudzabzala mbewu koma simudzakolola. Mudzaponda maolivi koma simudzadzola mafuta. Mudzaponda mphesa koma simudzamwa vinyo wotsekemera.*+