Yoswa 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa cha ana a Simiyoni chinali m’gawo la ana a Yuda chifukwa ana a Yuda gawo lawo linawakulira.+ Choncho ana a Simiyoni anapatsidwa malo pakati pa cholowa chawo.+
9 Cholowa cha ana a Simiyoni chinali m’gawo la ana a Yuda chifukwa ana a Yuda gawo lawo linawakulira.+ Choncho ana a Simiyoni anapatsidwa malo pakati pa cholowa chawo.+