Oweruza 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzapulumutsa anthu inu pogwiritsa ntchito amuna 300 amene anamwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani m’manja mwanu.+ Koma ena onsewa, aliyense abwerere kwawo.”
7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzapulumutsa anthu inu pogwiritsa ntchito amuna 300 amene anamwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani m’manja mwanu.+ Koma ena onsewa, aliyense abwerere kwawo.”