Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iye anali kugulula mawilo a magaleta awo moti anali kuwayendetsa movutikira.+ Pamenepo Aiguputo anayamba kunena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+

  • Deuteronomo 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+

  • 2 Mafumu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Nthawi yomweyo anthuwo ananyamuka n’kuyamba kuthawa kukungoyamba kumene kuda.+ Anasiya mahema awo, mahatchi awo,+ ndi abulu awo. Msasawo anausiya mmene unalili n’kuthawa kuti apulumutse miyoyo yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena