Oweruza 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno anatenga akulu a mzindawo, n’kutenganso mitengo yaminga ya m’chipululu ndi zitsamba zaminga. Atatero, anaonetsa amuna a ku Sukotiwo zoopsa.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
16 Ndiyeno anatenga akulu a mzindawo, n’kutenganso mitengo yaminga ya m’chipululu ndi zitsamba zaminga. Atatero, anaonetsa amuna a ku Sukotiwo zoopsa.+