Oweruza 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa,+ anaphimba chigwa chonse chifukwa cha kuchuluka kwawo ngati dzombe.+ Ngamila zawo+ zinali zosawerengeka, zochuluka ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja. Aheberi 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+
12 Tsopano Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa,+ anaphimba chigwa chonse chifukwa cha kuchuluka kwawo ngati dzombe.+ Ngamila zawo+ zinali zosawerengeka, zochuluka ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.
34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+