Oweruza 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana a Dani anatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe+ wake, ndipo anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu aphee ndi osatekeseka.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kutentha mzindawo ndi moto.+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
27 Ana a Dani anatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe+ wake, ndipo anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu aphee ndi osatekeseka.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kutentha mzindawo ndi moto.+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+