Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Asakhale m’dziko lako, kuti asakuchimwitse pamaso panga. Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe.”+

  • Oweruza 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ana a Isiraeli sanamvere ngakhale oweruza awo, koma anachita chiwerewere+ ndi milungu ina+ ndi kuigwadira. Iwo anapatuka mwamsanga panjira imene makolo awo anayendamo. Makolo awo anayenda m’njira imeneyo mwa kumvera malamulo a Yehova,+ koma iwo sanachite mofanana ndi makolo awo.

  • Salimo 106:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Iwo anakhala odetsedwa chifukwa cha ntchito zawo,+

      Zochita zawo zinawalowetsa m’makhalidwe oipa.+

  • Hoseya 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu anga amafunsira zinthu kwa mafano+ awo amtengo+ ndipo ndodo za m’manja mwawo zimawauza zochita. Amachita zimenezi chifukwa chakuti mtima wadama wawasocheretsa+ ndipo asiya kugonjera Mulungu wawo chifukwa cha damalo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena