Oweruza 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma a fuko la Yuda anayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati ndi kuwononga mzindawo.+ N’chifukwa chake mzindawo unatchedwa Horima.*+
17 Koma a fuko la Yuda anayendabe ndi abale awo a fuko la Simiyoni, ndipo anapha Akanani okhala ku Zefati ndi kuwononga mzindawo.+ N’chifukwa chake mzindawo unatchedwa Horima.*+