Oweruza 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7. Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7.
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+