Oweruza 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ana a Isiraeli anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anayamba kutumikira Abaala+ ndi mizati yopatulika.+ Salimo 106:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anayamba kutumikira mafano awo,+Ndipo mafanowo anakhala msampha wawo.+
7 Chotero ana a Isiraeli anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anayamba kutumikira Abaala+ ndi mizati yopatulika.+