Genesis 40:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe, mkulu wa operekera chikho uja anamuiwala Yosefe osam’kumbukira.+ Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+