Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa Abimeleki ndi kunyeketsa nzika za Sekemu ndi anthu a m’nyumba ya Milo,+ komanso moto+ utuluke mwa nzika za Sekemu ndi anthu a m’nyumba ya Milo ndi kunyeketsa Abimeleki.”+

  • Oweruza 9:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi mzindawo tsiku lonse, n’kuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo+ ndipo anaugwetsa+ n’kuthira mchere panthaka ya mzindawo.+

  • Oweruza 9:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Chotero anthu onsewo, aliyense wa iwo anadula nthambi yake ndi kutsatira Abimeleki. Kenako anatsamiritsa nthambizo pachipinda chotetezekacho n’kuchiyatsa moto, moti nawonso anthu onse okhala munsanja ya Sekemu, amuna ndi akazi pafupifupi 1,000, anafa.+

  • Yesaya 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nthaka ndidzaibwezera zoipa zake,+ ndipo anthu oipa ndidzawabwezera zolakwa zawo. Kunyada kwa anthu odzikuza ndidzakuthetsa, ndipo ndidzatsitsa olamulira ankhanza ndi odzikweza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena