Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.

  • Numeri 35:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+

  • Oweruza 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atatero anapita kunyumba ya bambo ake ku Ofira+ ndi kupha abale ake,+ ana aamuna 70 a Yerubaala, pamwala umodzi. Koma sanaphe Yotamu, mwana wamng’ono kwambiri mwa ana aamuna a Yerubaala, chifukwa anali atabisala.

  • 1 Mafumu 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ukatero, Yehova adzabwezeradi pamutu pake magazi ake,+ chifukwa anakantha amuna awiri olungama ndi abwino kuposa iyeyo,+ ndipo anawapha ndi lupanga. Anachita zimenezi Davide bambo anga osadziwa.+ Amuna ake anali Abineri+ mwana wa Nera mkulu wa asilikali a Isiraeli,+ ndi Amasa+ mwana wa Yeteri mkulu wa asilikali a Yuda.+

  • Salimo 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+

      Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+

  • Mateyu 23:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 kuti magazi onse olungama okhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu,+ kuyambira magazi a Abele+ wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena