Oweruza 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pambuyo pa Ehudi panadzakhala Samagara+ mwana wamwamuna wa Anati. Ameneyu anapha amuna achifilisiti+ 600 ndi chisonga chotosera ng’ombe pozitsogolera. Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.+
31 Pambuyo pa Ehudi panadzakhala Samagara+ mwana wamwamuna wa Anati. Ameneyu anapha amuna achifilisiti+ 600 ndi chisonga chotosera ng’ombe pozitsogolera. Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.+