Oweruza 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yefita anathawa chifukwa cha abale ake ndipo anakakhala m’dziko la Tobu.+ Kumeneko anthu osowa ntchito anali kusonkhana kwa Yefita ndi kupita naye limodzi kukaukira adani awo.+
3 Choncho Yefita anathawa chifukwa cha abale ake ndipo anakakhala m’dziko la Tobu.+ Kumeneko anthu osowa ntchito anali kusonkhana kwa Yefita ndi kupita naye limodzi kukaukira adani awo.+