Yoswa 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azithawira+ kumzinda umodzi mwa mizindayi n’kukaima pachipata+ cholowera mumzindawo. Akatero azifotokoza nkhani yake kwa akulu+ a mzindawo. Akuluwo amulandire n’kumupatsa malo mumzindamo kuti azikhala nawo limodzi. Oweruza 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali m’njira, anagwira mnyamata wa ku Sukoti+ amene anam’funsa mafunso.+ Pamenepo, mnyamatayo analembera Gidiyoni mayina okwana 77 a akalonga+ ndi akulu a mzinda wa Sukoti.
4 Azithawira+ kumzinda umodzi mwa mizindayi n’kukaima pachipata+ cholowera mumzindawo. Akatero azifotokoza nkhani yake kwa akulu+ a mzindawo. Akuluwo amulandire n’kumupatsa malo mumzindamo kuti azikhala nawo limodzi.
14 Ali m’njira, anagwira mnyamata wa ku Sukoti+ amene anam’funsa mafunso.+ Pamenepo, mnyamatayo analembera Gidiyoni mayina okwana 77 a akalonga+ ndi akulu a mzinda wa Sukoti.