Genesis 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Hamu anali Kusi,+ Miziraimu,+ Puti+ ndi Kanani.+ Deuteronomo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.
17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.