Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa, komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera m’thupi lake ndi mu mzimu wake. Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu za dziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.+

  • 1 Akorinto 7:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma ngati wina ndi wokhazikika mumtima mwake ndipo alibe chomuvutitsa, koma amatha kulamulira mtima wake, ndipo wasankha mumtima mwake kukhalabe wosakwatira,* wachita bwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena