Oweruza 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda ku Piratoni, m’dziko la Efuraimu, m’phiri la Aamaleki.+ 2 Samueli 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Benaya+ Mpiratoni, Hidai wa kuzigwa* za Gaasi,+ 1 Mbiri 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtsogoleri wa 11, wa mwezi wa 11, anali Benaya+ Mpiratoni, wochokera mwa ana a Efuraimu.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda ku Piratoni, m’dziko la Efuraimu, m’phiri la Aamaleki.+
14 Mtsogoleri wa 11, wa mwezi wa 11, anali Benaya+ Mpiratoni, wochokera mwa ana a Efuraimu.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.