Yoswa 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ku Sefela+ kunali Esitaoli,+ Zora,+ Asina, Yoswa 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Malire a gawo la cholowa chawo anadutsa ku Zora,+ Esitaoli, Iri-semesi, 2 Mbiri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zora,+ Aijaloni+ ndi Heburoni.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri imene inali ku Yuda ndi ku Benjamini.
10 Zora,+ Aijaloni+ ndi Heburoni.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri imene inali ku Yuda ndi ku Benjamini.