Genesis 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+ Genesis 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Isaki anali kupembedzera Yehova mosalekeza, makamaka chifukwa cha mkazi wake,+ popeza iye anali wosabereka.+ Yehova anamva kupembedzera kwake,+ ndipo Rabeka mkazi wakeyo anakhala ndi pakati. Luka 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo analibe mwana, chifukwa Elizabeti anali wosabereka,+ ndipo onse awiri anali okalamba.
16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+
21 Isaki anali kupembedzera Yehova mosalekeza, makamaka chifukwa cha mkazi wake,+ popeza iye anali wosabereka.+ Yehova anamva kupembedzera kwake,+ ndipo Rabeka mkazi wakeyo anakhala ndi pakati.