Oweruza 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+
5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+