Genesis 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anayankha kuti: “Ndidzakutumizira mwana wa mbuzi.” Koma mkaziyo anati: “Mundipatse chikole choti ndisunge kufikira pamene mudzaitumize.”+ 1 Samueli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Jese anatenga bulu, mkate, thumba lachikopa+ la vinyo ndi mwana wa mbuzi, ndipo anazitumiza kwa Sauli kudzera mwa Davide mwana wake.+ Luka 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Poyankha iye anauza bambo akewo kuti, ‘Ine zaka zonsezi ndakhala ndikukugwirirani ntchito ngati kapolo, ndipo sindinaphwanyepo malamulo anu n’kamodzi komwe, koma simunandipatseko ngakhale kamwana ka mbuzi kuti ndisangalale ndi mabwenzi anga.+
17 Iye anayankha kuti: “Ndidzakutumizira mwana wa mbuzi.” Koma mkaziyo anati: “Mundipatse chikole choti ndisunge kufikira pamene mudzaitumize.”+
20 Pamenepo Jese anatenga bulu, mkate, thumba lachikopa+ la vinyo ndi mwana wa mbuzi, ndipo anazitumiza kwa Sauli kudzera mwa Davide mwana wake.+
29 Poyankha iye anauza bambo akewo kuti, ‘Ine zaka zonsezi ndakhala ndikukugwirirani ntchito ngati kapolo, ndipo sindinaphwanyepo malamulo anu n’kamodzi komwe, koma simunandipatseko ngakhale kamwana ka mbuzi kuti ndisangalale ndi mabwenzi anga.+