Oweruza 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mkaziyo anapitiriza kulira pamaso pa Samisoni kwa masiku 7 a phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza.+ Kenako mkaziyo anaulula tanthauzo la mwambiwo kwa anthu a mtundu wake.+
17 Koma mkaziyo anapitiriza kulira pamaso pa Samisoni kwa masiku 7 a phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza.+ Kenako mkaziyo anaulula tanthauzo la mwambiwo kwa anthu a mtundu wake.+