Oweruza 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+ Oweruza 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+
4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+
5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+