Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko limene latsala ndi ili:+ Madera onse a Afilisiti+ ndi madera onse a Agesuri.+ Oweruza 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+
4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+